In 2014 Provoice collaborated with Award winning Hip Hop star GWAMBA and came up with the Nationwide hit Pokopoko. It took 3 solid years for the Knock It Boss to collaborate with another hip hop Artist on his song. Now he teams up with Macelba on his soon to be released song titled “Ankaseka”.
The new joint is to be released on the very same day Pokopoko dropped 3 years ago. Is history being repeated?
Produced by Cuff B of Big Vision Entertainment, Ankaseka, a dancehall and kwaito fusion beat will be officially released on Malawi-Music on 31st January 2017.
Below are the lyrics of this much anticipated jam by ProVoice:
INTRO
Knock it! Celba (yea) We here
HOOK
He he! Nthawi tinkayamba Ankaseka
He he! Pamene tinkayamba Ankaseka ankati
He he! Nthawi tikayamba Ankaseka
Ma man Ankaseka Maguy ankaphweketsa ankati Cha?
CHORUS
Ndife mafana Ndife mafana (Heeeeee!)
Ndife mafana Ndife mafana (Heee!)
Ndife mafana Ndife mafana
koma anaiwala chimodzi kuti mfana amakula (ankati cha?)
Ndife mafana Ndife mafana (Heeeee!)
Ndife mafana Ndife mafana (Heee!)
Ndife mafana Ndife mafana
anaiwala chimodzi kuti mfana amakula.
VERSE 1 (PROVOICE )
Pano pokha sindibisa ine ndinena chilungamo
Munkati Ndine kape pano bwanji mwaonano
Kupa ma beat nde sound ikumvekano
Mukanika kupanga Hit guys mulindi msephano
See de call me Dragon coz me spit fire
Pandekha ndimaima no Crew no Empire
Ah soh me run Dancehall from Lilongwe to Blantyre
Mi name quit Nonono never retire (You see it)
Nde ndizingophulisa kumangophulisa MABOMBA!!
Kundisuntha sizitheka ndili POMPA!!
Ndati ndizingophulisa MABOMBA! (Eish)
Kundisuntha sizitheka ndili POMPA!!
HOOK
CHORUS
VERSE 2 (MACELBA)
Look! Bongwe uja pano ndi Sir
Mfana uja lero ndi mdala
Aja munkati ndimadolo aja
Akateleka ngini amangophika phala
Nomwenu mesa munkandiseka (Huh!)
Mwaiwala zitseko munatseka (Huh!)
Nonse munkandionela pansi
Ndimaseka ndikuseka ndikakuonani pansi
Koma sorry ulendo uno sindikuluza (NO!)
Zanga zinayela ngati mkazi o user
Ndati sorry mesa iwe unkandiphwekesa
Lero ndakupepelesa ndine Macelba Mesa (Huh!!)
HOOK
CHORUS
VERSE 3 (PROVOICE)
Osaphweketsa don’t Despise anyone
Coz ah ting weh u av or weh ever u fram (en)
D most high gives ina right tym
Was ah lickle yut now turn ah big man (en)
Can’t u see pano takula (Grown)
We killin dem game en we giving dem Hits
Ina d streets me ah d real (Don)
Always on d road en we making d cheese
Remember munkanena kuti ineyo ndi mphale
Fans ikundikakamiza kuti ndituluse Chimbale
Nde ndizingophulitsa kumangophulitsa MABOMBA!!
Kundisuntha sizitheka ndili POMPA!!
HOOK
CHORUS