Zinthu 10 Zomwe Anthu Samadziwa Zokhudza Waxy K

0
4161
Share Button
  1. Kupatula Hip-hop Waxy K amaimbaso chamba cha RnB
  2. Alinso ndi luso loimba chida chilichonse chokhuzana ndi za nyimbo
  3. Ali ndi nyumba yomanga yekha yomwe amapangitsa rent
  4. Alibe azinzake opitilira asanu (5)
  5. Ali ndi mkazi m’modzi yekha yemweso anaonekera kale kwawo
  6. Akuti samasuta chamba kapenaso kumwa mowa
  7. Nyimbo amalemba pakati pa usiku ubongo uli fresh
  8. Ali ndi magalimoto awiri (Sienta ndi Vits) omwe amabweleketsa
  9. Amabwereketsaso ndalama za katapila
  10. Samayendayenda chifukwa amakhala busy kupanga practice daily
Share Button

LEAVE A REPLY

Please enter your comment!
Please enter your name here