Wikise Akudza Ndi Nyimbo Yatsopano Yotchedwa “Chikamphulikire”
Pa 1 August, oyimba wachinyamata otchedwa Wikise walengeza kuti akutulutsa nyimbo ina yatsopano yomwe akuitcha "Chikamphulikire". Malingana ndi Katswiriyu, Chikamphulikire ndi nyimbo yomwe ikudzudzula mabwana onse amene amachulutsa kukhomelera…